Oweruza 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kalekale mitengo inafuna kudzoza mfumu yawo. Pamenepo mitengoyo inauza mtengo wa maolivi+ kuti, ‘Iwe ukhale mfumu yathu.’+
8 “Kalekale mitengo inafuna kudzoza mfumu yawo. Pamenepo mitengoyo inauza mtengo wa maolivi+ kuti, ‘Iwe ukhale mfumu yathu.’+