2 Mbiri 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amaziya atasiya kutsatira Yehova, anthu anam’konzera chiwembu+ ku Yerusalemu. Patapita nthawi iye anathawira ku Lakisi.+ Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko n’kukamuphera komweko.+
27 Amaziya atasiya kutsatira Yehova, anthu anam’konzera chiwembu+ ku Yerusalemu. Patapita nthawi iye anathawira ku Lakisi.+ Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko n’kukamuphera komweko.+