2 Mafumu 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma atumiki+ a Yehoasi anagwirizana zom’chitira chiwembu+ ndipo anamupha panyumba+ ya Chimulu cha Dothi*+ panjira yotsetserekera ku Sila. 2 Mafumu 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mafumu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pomaliza pake, atumiki a mfumu Amoni anam’chitira chiwembu n’kumupha+ m’nyumba mwake momwe.
20 Koma atumiki+ a Yehoasi anagwirizana zom’chitira chiwembu+ ndipo anamupha panyumba+ ya Chimulu cha Dothi*+ panjira yotsetserekera ku Sila.
10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake.