2 Mbiri 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pomalizira pake, Uziya anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuika m’manda pamodzi ndi makolo ake, koma anamuika kunja kwa manda a mafumu+ chifukwa anati: “Ndi wakhate.” Kenako Yotamu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
23 Pomalizira pake, Uziya anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuika m’manda pamodzi ndi makolo ake, koma anamuika kunja kwa manda a mafumu+ chifukwa anati: “Ndi wakhate.” Kenako Yotamu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.