2 Mafumu 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake, Azariya anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anamuika m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Kenako Yotamu mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+
7 Pambuyo pake, Azariya anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anamuika m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Kenako Yotamu mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+