1 Mbiri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoasi anabereka Amaziya,+ Amaziya anabereka Azariya,+ Azariya anabereka Yotamu,+ 2 Mbiri 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhani zina zokhudza Yotamu,+ nkhondo zake ndi njira zake zonse, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda. Mateyu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uziya anabereka Yotamu.+Yotamu anabereka Ahazi.+Ahazi anabereka Hezekiya.+
7 Nkhani zina zokhudza Yotamu,+ nkhondo zake ndi njira zake zonse, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.