2 Mafumu 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera kudzaukira Yerusalemu mwankhondo ndipo anazungulira Ahazi koma sanathe kumenyana naye.+ Yesaya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno kunyumba ya Davide kunapita uthenga wakuti: “Dziko la Siriya layamba kudalira dziko la Efuraimu.”+ Choncho mtima wa Ahazi ndi wa anthu ake unayamba kunjenjemera, ngati mmene mitengo ya m’nkhalango imagwederera ndi mphepo.+
5 Pa nthawi imeneyo Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera kudzaukira Yerusalemu mwankhondo ndipo anazungulira Ahazi koma sanathe kumenyana naye.+
2 Ndiyeno kunyumba ya Davide kunapita uthenga wakuti: “Dziko la Siriya layamba kudalira dziko la Efuraimu.”+ Choncho mtima wa Ahazi ndi wa anthu ake unayamba kunjenjemera, ngati mmene mitengo ya m’nkhalango imagwederera ndi mphepo.+