1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda. 2 Mbiri 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nkhani zina+ zokhudza Ahazi, zoyambirira ndi zomalizira, ndiponso njira zake zonse, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda.
26 Nkhani zina+ zokhudza Ahazi, zoyambirira ndi zomalizira, ndiponso njira zake zonse, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.