Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Nkhani zina zokhudza Solomo ndi zonse zimene anachita, ndiponso nzeru zake, zinalembedwa m’buku lonena za Solomo.

  • 1 Mafumu 15:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Nkhani zina zonse zokhudza Asa, ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso zonse zimene anachita, ndi mizinda imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. Koma mu ukalamba wake,+ mapazi ake anachita matenda.+

  • 1 Mbiri 27:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yowabu+ mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize.+ Kenako mkwiyo+ wa Mulungu unagwera Isiraeli chifukwa chowerenga anthuwo, ndipo chiwerengerocho sichinalembedwe pa zochitika za m’masiku a Mfumu Davide.

  • 2 Mbiri 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu, zoyambirira ndi zomalizira,+ zinalembedwa m’mawu a mneneri Semaya+ ndiponso m’mawu a Ido+ wamasomphenya, motsatira mndandanda wa mayina a makolo. Nthawi zonse panali kuchitika nkhondo pakati pa Rehobowamu+ ndi Yerobowamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena