1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda. 2 Mbiri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nkhani zokhudza Asa, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda.
11 Nkhani zokhudza Asa, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.