1 Mafumu 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nkhani zina zonse zokhudza Asa, ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso zonse zimene anachita, ndi mizinda imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. Koma mu ukalamba wake,+ mapazi ake anachita matenda.+
23 Nkhani zina zonse zokhudza Asa, ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso zonse zimene anachita, ndi mizinda imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. Koma mu ukalamba wake,+ mapazi ake anachita matenda.+