1 Mbiri 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Yowabu sanawerenge+ a fuko la Levi+ ndi la Benjamini, chifukwa anali ataipidwa ndi mawu a mfumu.
6 Koma Yowabu sanawerenge+ a fuko la Levi+ ndi la Benjamini, chifukwa anali ataipidwa ndi mawu a mfumu.