Deuteronomo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+ Deuteronomo 32:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 anapitiriza kuwauza kuti: “Ganizirani mofatsa mawu onse amene ndikulankhula mokuchenjezani lero,+ ndipo muuze ana anu kuti aonetsetse kuti akuchita zimene mawu onse a chilamulo ichi akunena.+ Salimo 81:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Imvani anthu anga, ndipo ndidzakulangizani ndi kukuchenjezani.+Zikanakhala bwino ngati mukanandimvera, inu Aisiraeli.+
19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+
46 anapitiriza kuwauza kuti: “Ganizirani mofatsa mawu onse amene ndikulankhula mokuchenjezani lero,+ ndipo muuze ana anu kuti aonetsetse kuti akuchita zimene mawu onse a chilamulo ichi akunena.+
8 Imvani anthu anga, ndipo ndidzakulangizani ndi kukuchenjezani.+Zikanakhala bwino ngati mukanandimvera, inu Aisiraeli.+