Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake. Salimo 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndimvereni anthu anga, ndipo ine ndilankhula,+Inu Aisiraeli, ine ndipereka umboni wotsutsana nanu.+Ine ndine Mulungu, Mulungu wanu.+
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.
7 “Ndimvereni anthu anga, ndipo ine ndilankhula,+Inu Aisiraeli, ine ndipereka umboni wotsutsana nanu.+Ine ndine Mulungu, Mulungu wanu.+