Nehemiya 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma munaleza nawo mtima kwa zaka zambiri+ ndipo munapitirizabe kuwachenjeza+ mwa mzimu wanu potumiza aneneri anu, koma iwo sanamvere.+ Pamapeto pake munawapereka m’manja mwa mitundu ya anthu ya m’dzikolo.+
30 Koma munaleza nawo mtima kwa zaka zambiri+ ndipo munapitirizabe kuwachenjeza+ mwa mzimu wanu potumiza aneneri anu, koma iwo sanamvere.+ Pamapeto pake munawapereka m’manja mwa mitundu ya anthu ya m’dzikolo.+