1 Mbiri 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa ana a Elizafana+ panali Semaya+ mtsogoleri wawo ndi abale ake okwanira 200.