1 Mbiri 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwonjezera pa amenewa, Davide anaitanitsa Zadoki+ ndi Abiyatara,+ omwe anali ansembe. Anaitanitsanso Alevi awa: Uriyeli,+ Asaya,+ Yoweli,+ Semaya,+ Elieli,+ ndi Aminadabu.
11 Kuwonjezera pa amenewa, Davide anaitanitsa Zadoki+ ndi Abiyatara,+ omwe anali ansembe. Anaitanitsanso Alevi awa: Uriyeli,+ Asaya,+ Yoweli,+ Semaya,+ Elieli,+ ndi Aminadabu.