Mateyu 22:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Mukuganiza bwanji za Khristu? Kodi ndi mwana wa ndani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi mwana wa Davide.”+ Machitidwe 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa kwa akufa, osayembekezera kubwereranso kuthupi limene lingathe kuvunda, anaitchula motere, ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu kukoma mtima kwanga kosatha ndi kokhulupirika, kumene ndinasonyeza Davide.’+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+
42 “Mukuganiza bwanji za Khristu? Kodi ndi mwana wa ndani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi mwana wa Davide.”+
34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa kwa akufa, osayembekezera kubwereranso kuthupi limene lingathe kuvunda, anaitchula motere, ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu kukoma mtima kwanga kosatha ndi kokhulupirika, kumene ndinasonyeza Davide.’+
16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+