Salimo 99:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo atamande dzina lanu.+Dzina lanu ndi lalikulu, lochititsa mantha ndi loyera.+ Yohane 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atate lemekezani dzina lanu.” Pamenepo mawu+ anamveka kuchokera kumwamba kuti: “Ndalilemekeza ndipo ndidzalilemekezanso.”+
28 Atate lemekezani dzina lanu.” Pamenepo mawu+ anamveka kuchokera kumwamba kuti: “Ndalilemekeza ndipo ndidzalilemekezanso.”+