Genesis 36:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi amene anagonjetsa Amidiyani+ m’dziko la Mowabu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Aviti.+
35 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi amene anagonjetsa Amidiyani+ m’dziko la Mowabu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Aviti.+