1 Mbiri 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Patapita nthawi, Husamu anamwalira ndipo Hadadi+ mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani+ m’dziko la Mowabu, anayamba kulamulira m’malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Aviti.+
46 Patapita nthawi, Husamu anamwalira ndipo Hadadi+ mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani+ m’dziko la Mowabu, anayamba kulamulira m’malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Aviti.+