2 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pambuyo pake, mfumu ya ana a Amoni+ inamwalira, ndipo Hanuni mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwa bambo ake.+
10 Pambuyo pake, mfumu ya ana a Amoni+ inamwalira, ndipo Hanuni mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwa bambo ake.+