2 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mfumu ya Aamoni+ inamwalira, ndipo mwana wake Hanuni anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+