Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.

  • Oweruza 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+

  • Oweruza 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako Yefita anatumiza mithenga kwa mfumu ya ana a Amoni+ kuti: “Ndili nanu chiyani inu,+ kuti mubwere kudzamenyana nane m’dziko langa?”

  • Oweruza 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Iye anakantha ana a Amoni kuyambira ku Aroweli mpaka kukafika ku Miniti,+ mizinda 20. Anawakantha koopsa mpaka kukafika ku Abele-kerami. Choncho ana a Amoni anagonja pamaso pa ana a Isiraeli.

  • 1 Samueli 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Nahasi Muamoni+ anapita kukamanga msasa kuti amenyane ndi mzinda wa Yabesi+ ku Giliyadi. Zitatero, amuna onse a ku Yabesi anauza Nahasi kuti: “Chita nafe pangano kuti tizikutumikira.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena