Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero. Oweruza 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita nthawi, ana a Amoni+ anasonkhanitsidwa pamodzi ndipo anamanga msasa wawo ku Giliyadi.+ Zitatero, ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi ndi kumanga msasa wawo ku Mizipa.+
38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.
17 Patapita nthawi, ana a Amoni+ anasonkhanitsidwa pamodzi ndipo anamanga msasa wawo ku Giliyadi.+ Zitatero, ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi ndi kumanga msasa wawo ku Mizipa.+