2 Samueli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno anamuuza kuti: “Asiriya akandiposa mphamvu, iweyo undipulumutse. Koma ana a Amoni akakukulira mphamvu, ineyo ndifika kudzakupulumutsa.+
11 Ndiyeno anamuuza kuti: “Asiriya akandiposa mphamvu, iweyo undipulumutse. Koma ana a Amoni akakukulira mphamvu, ineyo ndifika kudzakupulumutsa.+