1 Mbiri 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno anamuuza kuti: “Asiriya+ akandiposa mphamvu, iweyo undipulumutse.+ Koma ana a Amoni akakukulira mphamvu, ineyo ndifika kudzakupulumutsa.+ Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
12 Ndiyeno anamuuza kuti: “Asiriya+ akandiposa mphamvu, iweyo undipulumutse.+ Koma ana a Amoni akakukulira mphamvu, ineyo ndifika kudzakupulumutsa.+
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+