2 Samueli 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Yowabu anauza mfumu kuti: “Yehova Mulungu wanu awonjezere anthu kuwirikiza nthawi 100 pa kuchuluka kwawo, maso anu inu mbuyanga mfumu akuona. Koma inu mbuyanga mfumu, n’chifukwa chiyani mukufuna kuchita zimenezi?”+
3 Koma Yowabu anauza mfumu kuti: “Yehova Mulungu wanu awonjezere anthu kuwirikiza nthawi 100 pa kuchuluka kwawo, maso anu inu mbuyanga mfumu akuona. Koma inu mbuyanga mfumu, n’chifukwa chiyani mukufuna kuchita zimenezi?”+