Ekisodo 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo, Yehova anayamba kumva chisoni chifukwa cha tsoka limene ananena kuti agwetsera anthu ake.+ Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.
14 Pamenepo, Yehova anayamba kumva chisoni chifukwa cha tsoka limene ananena kuti agwetsera anthu ake.+
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.