Numeri 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano Yehova anatsegula maso a Balamu,+ ndipo iye anaona mngelo wa Yehova ali chilili panjirapo, lupanga lili m’manja. Nthawi yomweyo, Balamu anagwada pansi n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.
31 Tsopano Yehova anatsegula maso a Balamu,+ ndipo iye anaona mngelo wa Yehova ali chilili panjirapo, lupanga lili m’manja. Nthawi yomweyo, Balamu anagwada pansi n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.