1 Mafumu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Yehova Mulungu wanga, mwaika mtumiki wanune kukhala mfumu m’malo mwa Davide bambo anga. Komatu ndine mwana+ ndipo sindikudziwa zinthu zambiri.+ 1 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano mfumu Davide inauza mpingo wonse+ kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamng’ono+ ndi wosakhwima. Koma ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa chinyumba chachikuluchi, si cha munthu ayi,+ koma ndi cha Yehova Mulungu.
7 Tsopano Yehova Mulungu wanga, mwaika mtumiki wanune kukhala mfumu m’malo mwa Davide bambo anga. Komatu ndine mwana+ ndipo sindikudziwa zinthu zambiri.+
29 Tsopano mfumu Davide inauza mpingo wonse+ kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamng’ono+ ndi wosakhwima. Koma ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa chinyumba chachikuluchi, si cha munthu ayi,+ koma ndi cha Yehova Mulungu.