1 Mafumu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mfumu Davide anali atakalamba+ ndipo anali ndi zaka zambiri. Ankamufunditsa zovala koma sankamva kutentha.
1 Mfumu Davide anali atakalamba+ ndipo anali ndi zaka zambiri. Ankamufunditsa zovala koma sankamva kutentha.