1 Mbiri 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa ana a Ladani,+ panali Yehieli.+ Ana amenewo anali mbadwa za Agerisoni kudzera mwa Ladani, ndipo anali atsogoleri a nyumba za makolo za Ladani Mgerisoni.
21 Pa ana a Ladani,+ panali Yehieli.+ Ana amenewo anali mbadwa za Agerisoni kudzera mwa Ladani, ndipo anali atsogoleri a nyumba za makolo za Ladani Mgerisoni.