Levitiko 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Aroni anakweza manja ake pa anthuwo ndi kuwadalitsa.+ Atatero, anatsika+ kuguwa lansembe kumene anali atapereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere:
22 Kenako Aroni anakweza manja ake pa anthuwo ndi kuwadalitsa.+ Atatero, anatsika+ kuguwa lansembe kumene anali atapereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zachiyanjano.