Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere:

  • Deuteronomo 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+

  • Deuteronomo 21:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+

  • 1 Mbiri 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana aamuna a Amuramu anali Aroni+ ndi Mose.+ Koma Aroni anapatulidwa+ kuti iye ndi ana ake aziyeretsa Malo Oyera Koposa,+ mpaka kalekale. Komanso kuti azifukiza nsembe+ yautsi pamaso pa Yehova, kumutumikira,+ ndi kupereka madalitso+ m’dzina lake mpaka kalekale.

  • Luka 24:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Pamenepo anawatsogolera kupita nawo ku Betaniya. Kumeneko anakweza manja ake ndi kuwadalitsa.+

  • Machitidwe 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba anamutumiza kwa inu,+ kuti adzakudalitseni mwa kubweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.”

  • Aheberi 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano, palibe angatsutse kuti wamng’ono amadalitsidwa ndi wamkulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena