Nehemiya 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho ansembe ndi Alevi pamodzi ndi oimba+ ndi alonda a pazipata+ anayamba kusamalira udindo+ wawo kwa Mulungu ndi kusunga lamulo lakuti azikhala oyera,+ malinga ndi lamulo la Davide ndi mwana wake Solomo.
45 Choncho ansembe ndi Alevi pamodzi ndi oimba+ ndi alonda a pazipata+ anayamba kusamalira udindo+ wawo kwa Mulungu ndi kusunga lamulo lakuti azikhala oyera,+ malinga ndi lamulo la Davide ndi mwana wake Solomo.