7 Chotero iwo anapereka golide wokwanira matalente 5,000, madariki 10,000, siliva wokwanira matalente 10,000, mkuwa wokwanira matalente 18,000, ndi zitsulo zokwanira matalente 100,000.+ Anapereka zonsezi kuti zigwire ntchito panyumba ya Mulungu woona.