2 Akorinto 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu akukudalitsani m’njira iliyonse kuti muthe kupereka mowolowa manja m’njira zosiyanasiyana, ndipo kudzera m’zochita zathu, kuwolowa manja koteroko kukuchititsa anthu kuyamika Mulunguyo.+
11 Mulungu akukudalitsani m’njira iliyonse kuti muthe kupereka mowolowa manja m’njira zosiyanasiyana, ndipo kudzera m’zochita zathu, kuwolowa manja koteroko kukuchititsa anthu kuyamika Mulunguyo.+