2 Akorinto 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inunso mungathandizepo mwa kutiperekera mapembedzero anu,+ kuti pakhale anthu ambiri otiperekera mapemphero oyamikira+ zinthu zimene tapatsidwa mokoma mtima, chifukwa cha mapemphero a anthu ambiri.+ 2 Akorinto 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti zonsezi zachitika chifukwa cha ubwino wanu.+ Ndiponso zachitika kuti kukoma mtima kwakukulu kumene kunawonjezeka kuchulukebe chifukwa cha anthu ambiri amene akupereka mapemphero oyamikira, zimene zikuchititsa kuti Mulungu alandire ulemerero.+
11 Inunso mungathandizepo mwa kutiperekera mapembedzero anu,+ kuti pakhale anthu ambiri otiperekera mapemphero oyamikira+ zinthu zimene tapatsidwa mokoma mtima, chifukwa cha mapemphero a anthu ambiri.+
15 Pakuti zonsezi zachitika chifukwa cha ubwino wanu.+ Ndiponso zachitika kuti kukoma mtima kwakukulu kumene kunawonjezeka kuchulukebe chifukwa cha anthu ambiri amene akupereka mapemphero oyamikira, zimene zikuchititsa kuti Mulungu alandire ulemerero.+