Nehemiya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Panalinso Sabetai+ ndi Yozabadi,+ mwa atsogoleri a Alevi. Amenewa anali kuyang’anira ntchito ya panja pa nyumba ya Mulungu woona.
16 Panalinso Sabetai+ ndi Yozabadi,+ mwa atsogoleri a Alevi. Amenewa anali kuyang’anira ntchito ya panja pa nyumba ya Mulungu woona.