-
Ezara 8:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Pa tsiku lachinayi tinayeza siliva, golide+ ndi ziwiya+ zija m’nyumba ya Mulungu wathu. Titatero tinapereka zinthuzo m’manja mwa wansembe Meremoti+ mwana wa Uliya, yemwe anali limodzi ndi Eleazara mwana wa Pinihasi. Iwowa anali limodzi ndi Yozabadi+ mwana wa Yesuwa ndi Nowadiya mwana wa Binui,+ omwe anali Alevi.
-