-
Nehemiya 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno Meremoti+ mwana wamwamuna wa Uliya,+ mwana wamwamuna wa Hakozi, anakonza mpandawo kuchokera pamene ana aamuna a Haseneya analekezera. Kenako, Mesulamu+ mwana wamwamuna wa Berekiya, mwana wamwamuna wa Mesezabele, anakonza mpandawo kuchokera pamene Meremoti analekezera. Kenako, Zadoki mwana wamwamuna wa Baana, anakonza mpandawo kuchokera pamene Mesulamu analekezera.
-