Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 3:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Hananiya mwana wamwamuna wa Selemiya ndi Hanuni mwana wamwamuna wa 6 wa Zalafi, anakonzanso chigawo china cha mpanda.

      Kenako Mesulamu+ mwana wamwamuna wa Berekiya, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba* yake kuchokera pamene winayo analekezera.+

  • Nehemiya 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti anthu ambiri mu Yuda anamulumbirira kukhala naye mwamtendere chifukwa anali mkamwini wa Sekaniya, mwana wamwamuna wa Ara.+ Ndipo Yehohanani mwana wamwamuna wa Tobia, anakwatira mwana wamkazi wa Mesulamu,+ mwana wamwamuna wa Berekiya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena