2 Samueli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anali ndi zaka 30 pamene anakhala mfumu. Iye analamulira monga mfumu kwa zaka 40.+ 1 Mbiri 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Masiku onse amene iye analamulira Isiraeli anakwana zaka 40.+ Ku Heburoni analamulira zaka 7,+ ndipo ku Yerusalemu analamulira zaka 33.+
27 Masiku onse amene iye analamulira Isiraeli anakwana zaka 40.+ Ku Heburoni analamulira zaka 7,+ ndipo ku Yerusalemu analamulira zaka 33.+