2 Samueli 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Womutsatira anali Eleazara+ mwana wa Dodo+ mwana wa Ahohi. Iye anali mmodzi mwa amuna atatu amphamvu amene anali ndi Davide pamene anatonza Afilisiti. Iwo anasonkhana kumeneko kuti amenye nkhondo, ndipo amuna a Isiraeli anali atathawa.+ 1 Mbiri 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wotsatira wake anali Eleazara+ mwana wa Dodo, Muahohi.+ Iye anali mmodzi wa amuna atatu amphamvuwo.+
9 Womutsatira anali Eleazara+ mwana wa Dodo+ mwana wa Ahohi. Iye anali mmodzi mwa amuna atatu amphamvu amene anali ndi Davide pamene anatonza Afilisiti. Iwo anasonkhana kumeneko kuti amenye nkhondo, ndipo amuna a Isiraeli anali atathawa.+
12 Wotsatira wake anali Eleazara+ mwana wa Dodo, Muahohi.+ Iye anali mmodzi wa amuna atatu amphamvuwo.+