Oweruza 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda ku Piratoni, m’dziko la Efuraimu, m’phiri la Aamaleki.+
15 Kenako Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda ku Piratoni, m’dziko la Efuraimu, m’phiri la Aamaleki.+