Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 36:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Elifazi mwana wa Esau anali ndi mdzakazi dzina lake Timina.+ Patapita nthawi, mdzakaziyu anaberekera Elifazi mwana wamwamuna dzina lake Amaleki.+ Amenewa ndiwo anali ana a Ada mkazi wa Esau.

  • Ekisodo 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 ndipo anati: “Popeza dzanja laukira mpando wachifumu+ wa Ya,+ Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo.”+

  • Numeri 13:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Aamaleki+ amakhala ku Negebu.+ Ahiti, Ayebusi+ ndi Aamori+ amakhala kudera lamapiri. Akanani+ amakhala m’mphepete mwa nyanja, ndi m’mphepete mwa mtsinje wa Yorodano.”

  • 1 Samueli 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova wa makamu+ wanena kuti, ‘Ndibwezera+ Aamaleki chifukwa choukira Aisiraeli panjira, pamene Aisiraeliwo anali kutuluka mu Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena