1 Mafumu 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo Solomo anapereka kwa Hiramu tirigu wokwana miyezo 20,000 ya kori,*+ kuti chikhale chakudya cha banja lake, ndiponso mafuta oyenga bwino kwambiri+ okwana miyezo 20 ya kori. Izi n’zimene Solomo ankapereka kwa Hiramu chaka ndi chaka.+ 2 Mbiri 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anamanganso mosungira+ mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta, ndipo anamanganso makola+ a zinyama zonse zosiyanasiyana ndi a magulu a ziweto.
11 Ndipo Solomo anapereka kwa Hiramu tirigu wokwana miyezo 20,000 ya kori,*+ kuti chikhale chakudya cha banja lake, ndiponso mafuta oyenga bwino kwambiri+ okwana miyezo 20 ya kori. Izi n’zimene Solomo ankapereka kwa Hiramu chaka ndi chaka.+
28 Anamanganso mosungira+ mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta, ndipo anamanganso makola+ a zinyama zonse zosiyanasiyana ndi a magulu a ziweto.