6 Anamanganso Baalati+ ndi mizinda yonse yosungirako zinthu imene inakhala ya Solomo, mizinda yonse yosungirako magaleta,+ mizinda yonse ya amuna okwera pamahatchi,+ ndi chilichonse chimene iye anakonda+ kumanga ku Yerusalemu, ku Lebanoni,+ ndi m’dziko lonse limene ankalamulira.