1 Mbiri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uwu ndiwo mndandanda wa amuna amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mwana wa Mhakimoni, yemwe anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 300 ulendo umodzi.+
11 Uwu ndiwo mndandanda wa amuna amphamvu a Davide: Yasobeamu+ mwana wa Mhakimoni, yemwe anali mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 300 ulendo umodzi.+